Mateyu 13:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiye kunabwera akapolo a mwinimunda uja kudzamuuza kuti, ‘Mbuye, kodi simunafese mbewu zabwino m’munda wanuwu?+ Nanga namsongoleyu wachokeranso kuti?’+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:27 Nsanja ya Olonda,7/15/2013, tsa. 10
27 Ndiye kunabwera akapolo a mwinimunda uja kudzamuuza kuti, ‘Mbuye, kodi simunafese mbewu zabwino m’munda wanuwu?+ Nanga namsongoleyu wachokeranso kuti?’+