Mateyu 13:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 kuti zikwaniritsidwe zimene zinanenedwa kudzera mwa mneneri amene anati: “Ndidzatsegula pakamwa panga ndi kunena mafanizo, ndidzafalitsa zinthu zobisika kuchokera pa chiyambi cha dziko lapansi.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:35 “Wotsatira Wanga,” tsa. 119 Nsanja ya Olonda,8/15/2011, tsa. 119/1/2002, ptsa. 13-14
35 kuti zikwaniritsidwe zimene zinanenedwa kudzera mwa mneneri amene anati: “Ndidzatsegula pakamwa panga ndi kunena mafanizo, ndidzafalitsa zinthu zobisika kuchokera pa chiyambi cha dziko lapansi.”+