Mateyu 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma ophunzirawo anamuuza kuti: “Kopanda anthu ngati kuno tiipeza kuti mitanda ya mkate yokwanira khamu lonseli?”+
33 Koma ophunzirawo anamuuza kuti: “Kopanda anthu ngati kuno tiipeza kuti mitanda ya mkate yokwanira khamu lonseli?”+