Mateyu 15:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Anthu onsewo anadya ndi kukhuta, moti zotsala zimene anatolera zinadzaza madengu akuluakulu 7.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:37 Nsanja ya Olonda,12/1/1987, tsa. 8