Mateyu 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kapolo mnzakeyo anagwada pansi ndi kuyamba kumudandaulira kuti, ‘Mundilezereko mtima chonde,+ ndidzakubwezerani.’
29 Kapolo mnzakeyo anagwada pansi ndi kuyamba kumudandaulira kuti, ‘Mundilezereko mtima chonde,+ ndidzakubwezerani.’