Mateyu 18:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kodi nawenso sukanam’chitira chifundo+ kapolo mnzako, monga momwe ine ndinakuchitira chifundo?’+