Mateyu 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Pakuti ufumu wakumwamba uli ngati mwinimunda wa mpesa, amene analawirira m’mawa kwambiri kukafuna anthu aganyu kuti akagwire ntchito m’munda wake wa mpesa.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:1 Yesu—Ndi Njira, tsa. 226 Nsanja ya Olonda,8/15/1989, tsa. 8
20 “Pakuti ufumu wakumwamba uli ngati mwinimunda wa mpesa, amene analawirira m’mawa kwambiri kukafuna anthu aganyu kuti akagwire ntchito m’munda wake wa mpesa.+