Mateyu 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero iwo anapita. Pafupifupi 12 koloko+ ndi 3 koloko masana,*+ mwinimunda uja anapitanso kukachita chimodzimodzi. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:5 Yesu—Ndi Njira, tsa. 226 Nsanja ya Olonda,8/15/1989, tsa. 8
5 Chotero iwo anapita. Pafupifupi 12 koloko+ ndi 3 koloko masana,*+ mwinimunda uja anapitanso kukachita chimodzimodzi.