-
Mateyu 20:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Chotero oyambirira aja atafika, anaganiza kuti alandira zambiri, koma nawonso malipiro amene analandira anali dinari imodzi.
-