Mateyu 20:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Yesu anayankha kuti: “Anthu inu simukudziwa chimene mukupempha. Kodi mungamwe+ zimene ine ndatsala pang’ono kumwa?” Iwo anati: “Inde tingamwe.” Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:22 Yesu—Ndi Njira, tsa. 229 Nsanja ya Olonda,9/1/1989, tsa. 8
22 Koma Yesu anayankha kuti: “Anthu inu simukudziwa chimene mukupempha. Kodi mungamwe+ zimene ine ndatsala pang’ono kumwa?” Iwo anati: “Inde tingamwe.”