Mateyu 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo anabweretsa bulu uja limodzi ndi mwana wake wamphongo. Kenako anayala malaya awo akunja pa abuluwo ndipo iye anakwerapo.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:7 Yesu—Ndi Njira, tsa. 238 Nsanja ya Olonda,3/1/1997, ptsa. 30-3111/1/1989, tsa. 8
7 Iwo anabweretsa bulu uja limodzi ndi mwana wake wamphongo. Kenako anayala malaya awo akunja pa abuluwo ndipo iye anakwerapo.+