Mateyu 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ophunzira aja ataona zimenezi, anadabwa ndi kunena kuti: “Zatheka bwanji kuti mkuyuwu ufote nthawi yomweyi?”+
20 Ophunzira aja ataona zimenezi, anadabwa ndi kunena kuti: “Zatheka bwanji kuti mkuyuwu ufote nthawi yomweyi?”+