Mateyu 21:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndani mwa ana awiriwa amene anachita chifuniro cha bambo ake?”+ Iwo anati: “Wachiwiriyu.” Yesu anawauza kuti: “Ndithu ndikukuuzani kuti okhometsa msonkho ndi mahule akukusiyani m’mbuyo n’kukalowa mu ufumu wa Mulungu. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:31 Yesu—Ndi Njira, tsa. 246 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, ptsa. 28-291/1/1990, tsa. 8
31 Ndani mwa ana awiriwa amene anachita chifuniro cha bambo ake?”+ Iwo anati: “Wachiwiriyu.” Yesu anawauza kuti: “Ndithu ndikukuuzani kuti okhometsa msonkho ndi mahule akukusiyani m’mbuyo n’kukalowa mu ufumu wa Mulungu.