Mateyu 21:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Iwo anayankha kuti: “Chifukwa chakuti ndi oipa, adzawawononga koopsa+ ndipo munda wa mpesawo adzaupereka kwa alimi ena, amene angam’patse zipatso m’nyengo yake.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:41 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 246-247 Nsanja ya Olonda,1/1/1990, ptsa. 8-9
41 Iwo anayankha kuti: “Chifukwa chakuti ndi oipa, adzawawononga koopsa+ ndipo munda wa mpesawo adzaupereka kwa alimi ena, amene angam’patse zipatso m’nyengo yake.”+