Mateyu 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Pamene mfumu ija inalowa kukayendera alendowo, inaona munthu wina mmenemo amene sanavale chovala chaukwati.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:11 Nsanja ya Olonda,1/15/1990, tsa. 9
11 “Pamene mfumu ija inalowa kukayendera alendowo, inaona munthu wina mmenemo amene sanavale chovala chaukwati.+