Mateyu 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano Yesu anayamba ulendo kuchoka kukachisiko. Kenako ophunzira ake anabwera pafupi naye kuti amuonetse nyumba za pakachisipo.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:1 Yesu—Ndi Njira, tsa. 255 Nsanja ya Olonda,3/1/1990, tsa. 25
24 Tsopano Yesu anayamba ulendo kuchoka kukachisiko. Kenako ophunzira ake anabwera pafupi naye kuti amuonetse nyumba za pakachisipo.+