Mateyu 24:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Chotero munthu akadzakuuzani kuti, ‘Onani! Khristu uja ali kuno,’+ kapena, ‘Ali uko!’ musadzakhulupirire zimenezo.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:23 Nsanja ya Olonda,2/15/1994, ptsa. 11-12
23 “Chotero munthu akadzakuuzani kuti, ‘Onani! Khristu uja ali kuno,’+ kapena, ‘Ali uko!’ musadzakhulupirire zimenezo.+