Mateyu 24:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “Tsopano phunzirani mfundo imeneyi pa fanizo ili la mkuyu: Nthambi yake yanthete ikaphuka ndi kuchita masamba, mumadziwa kuti dzinja lili pafupi.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:32 Yesu—Ndi Njira, tsa. 258 Nsanja ya Olonda,5/15/2003, tsa. 264/1/1990, tsa. 25
32 “Tsopano phunzirani mfundo imeneyi pa fanizo ili la mkuyu: Nthambi yake yanthete ikaphuka ndi kuchita masamba, mumadziwa kuti dzinja lili pafupi.+