Mateyu 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa nthawiyi, ansembe aakulu ndiponso akulu anasonkhana m’bwalo lamkati kunyumba ya mkulu wa ansembe wotchedwa Kayafa.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:3 Yesu—Ndi Njira, tsa. 266 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, ptsa. 8-9
3 Pa nthawiyi, ansembe aakulu ndiponso akulu anasonkhana m’bwalo lamkati kunyumba ya mkulu wa ansembe wotchedwa Kayafa.+