Mateyu 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Osaukawo muli nawo nthawi zonse,+ koma ine simudzakhala nane nthawi zonse.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:11 Nsanja ya Olonda,6/15/2015, tsa. 511/1/2005, ptsa. 6-7 Galamukani!,6/8/1998, ptsa. 8-9