Mateyu 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndithu ndikukuuzani, Kulikonse kumene uthenga wabwinowu udzalalikidwe m’dziko lonse, anthu azidzanena zimene mayiyu wachita kuti azidzam’kumbukira.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:13 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,12/2017, tsa. 5
13 Ndithu ndikukuuzani, Kulikonse kumene uthenga wabwinowu udzalalikidwe m’dziko lonse, anthu azidzanena zimene mayiyu wachita kuti azidzam’kumbukira.”+