Mateyu 26:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Apa n’kuti womupereka ameneyu atawapatsa chizindikiro chakuti: “Amene ndim’psompsone ndi ameneyo, mum’gwire.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:48 Yesu—Ndi Njira, tsa. 284 Nsanja ya Olonda,10/15/1990, tsa. 8
48 Apa n’kuti womupereka ameneyu atawapatsa chizindikiro chakuti: “Amene ndim’psompsone ndi ameneyo, mum’gwire.”+