Mateyu 26:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Koma Petulo anali kumutsatirabe chapatali ndithu, mpaka anafika m’bwalo lamkati+ kunyumba ya mkulu wa ansembeyo. Atalowa mkatimo, anakhala pansi pamodzi ndi antchito a m’nyumbamo kuti aone zotsatira zake.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:58 Yesu—Ndi Njira, tsa. 288 Tsanzirani, ptsa. 199-200 Nsanja ya Olonda,4/1/2010, ptsa. 22-2311/15/1990, tsa. 8
58 Koma Petulo anali kumutsatirabe chapatali ndithu, mpaka anafika m’bwalo lamkati+ kunyumba ya mkulu wa ansembeyo. Atalowa mkatimo, anakhala pansi pamodzi ndi antchito a m’nyumbamo kuti aone zotsatira zake.+
26:58 Yesu—Ndi Njira, tsa. 288 Tsanzirani, ptsa. 199-200 Nsanja ya Olonda,4/1/2010, ptsa. 22-2311/15/1990, tsa. 8