Mateyu 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo Yudasi amene anam’pereka uja ataona kuti Yesu waweruzidwa kuti aphedwe, anavutika koopsa mumtima mwake moti anapita kukabweza ndalama 30+ zasiliva zija kwa ansembe aakulu ndiponso akulu. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:3 Nsanja ya Olonda,1/15/2008, tsa. 31
3 Pamenepo Yudasi amene anam’pereka uja ataona kuti Yesu waweruzidwa kuti aphedwe, anavutika koopsa mumtima mwake moti anapita kukabweza ndalama 30+ zasiliva zija kwa ansembe aakulu ndiponso akulu.