-
Mateyu 27:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Koma ansembe aakulu anatenga ndalama zasilivazo n’kunena kuti: “N’kosaloleka kuponya ndalamazi m’malo opatulika osungiramo chuma, chifukwa ndi malipiro a magazi.”
-