Mateyu 27:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Poona kuti sizikuthandiza, komanso pakuyambika chipolowe, Pilato anangotenga madzi+ ndi kusamba m’manja pamaso pa khamu la anthulo, n’kunena kuti: “Inetu ndasamba m’manja, ndilibe mlandu wa magazi a munthu uyu. Zonse zili kwa inu.” Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:24 Nsanja ya Olonda,9/15/2005, tsa. 12
24 Poona kuti sizikuthandiza, komanso pakuyambika chipolowe, Pilato anangotenga madzi+ ndi kusamba m’manja pamaso pa khamu la anthulo, n’kunena kuti: “Inetu ndasamba m’manja, ndilibe mlandu wa magazi a munthu uyu. Zonse zili kwa inu.”