Mateyu 27:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Komanso analuka chisoti chachifumu chaminga ndi kumuveka kumutu n’kumupatsa bango m’dzanja lake lamanja. Kenako anamugwadira ndi kum’chitira zachipongwe+ kuti: “Mtendere ukhale nanu, inu Mfumu ya Ayuda!”+
29 Komanso analuka chisoti chachifumu chaminga ndi kumuveka kumutu n’kumupatsa bango m’dzanja lake lamanja. Kenako anamugwadira ndi kum’chitira zachipongwe+ kuti: “Mtendere ukhale nanu, inu Mfumu ya Ayuda!”+