Mateyu 27:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Atamaliza kumuchitira zachipongwezo,+ anamuvula chinsalu chija ndi kumuveka malaya ake akunja n’kupita naye kukamupachika.+
31 Atamaliza kumuchitira zachipongwezo,+ anamuvula chinsalu chija ndi kumuveka malaya ake akunja n’kupita naye kukamupachika.+