Mateyu 27:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pamene anali kupita, anakumana ndi Simoni, nzika ya ku Kurene.+ Iwo anasenzetsa munthu ameneyu mtengo wozunzikirapo* wa Yesu. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:32 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 296-297 Nsanja ya Olonda,7/15/1992, tsa. 6
32 Pamene anali kupita, anakumana ndi Simoni, nzika ya ku Kurene.+ Iwo anasenzetsa munthu ameneyu mtengo wozunzikirapo* wa Yesu.