Mateyu 27:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Komanso pamwamba pa mutu wake anakhomapo chikwangwani cha mawu osonyeza mlandu wake kuti: “Uyu ndi Yesu, Mfumu ya Ayuda.”+
37 Komanso pamwamba pa mutu wake anakhomapo chikwangwani cha mawu osonyeza mlandu wake kuti: “Uyu ndi Yesu, Mfumu ya Ayuda.”+