Mateyu 27:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Komanso akazi ambiri ochokera ku Galileya amene ankatsatira Yesu kuti azimutumikira,+ anali komweko akuonerera chapatali ndithu.+
55 Komanso akazi ambiri ochokera ku Galileya amene ankatsatira Yesu kuti azimutumikira,+ anali komweko akuonerera chapatali ndithu.+