Mateyu 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atafika pafupi, anazindikira kuti pachitika chivomezi champhamvu, pakuti mngelo wa Yehova anatsika kumwamba, ndipo anafika ndi kugubuduza chimwala chija, n’kukhala pachimwalapo.+
2 Atafika pafupi, anazindikira kuti pachitika chivomezi champhamvu, pakuti mngelo wa Yehova anatsika kumwamba, ndipo anafika ndi kugubuduza chimwala chija, n’kukhala pachimwalapo.+