Mateyu 28:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ansembe aakuluwo atakambirana ndi akulu, anapangana zochita ndipo anapereka ndalama zasiliva zambiri kwa asilikaliwo+
12 Ansembe aakuluwo atakambirana ndi akulu, anapangana zochita ndipo anapereka ndalama zasiliva zambiri kwa asilikaliwo+