Maliko 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Monga mmene analembera m’buku la mneneri Yesaya kuti: “(Taona! Ine ndikutumiza mthenga wanga pamaso pako, amene adzakonza njira yako.)*+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:2 Nsanja ya Olonda,6/15/1987, tsa. 12
2 Monga mmene analembera m’buku la mneneri Yesaya kuti: “(Taona! Ine ndikutumiza mthenga wanga pamaso pako, amene adzakonza njira yako.)*+