Maliko 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nthawi yomweyo iwo anatuluka m’sunagogemo ndi kupita kunyumba kwa Simoni+ ndi Andireya. Yakobo ndi Yohane nawonso anapita nawo.
29 Nthawi yomweyo iwo anatuluka m’sunagogemo ndi kupita kunyumba kwa Simoni+ ndi Andireya. Yakobo ndi Yohane nawonso anapita nawo.