Maliko 1:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma iye anawayankha kuti: “Tiyeni tipite kwina kumidzi yapafupi, kuti ndikalalikire+ kumenekonso, pakuti ndicho cholinga chimene ndinabwerera.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:38 Yesu—Ndi Njira, tsa. 62 Galamukani!,8/8/2001, tsa. 20 Nsanja ya Olonda,4/1/1986, ptsa. 8-21
38 Koma iye anawayankha kuti: “Tiyeni tipite kwina kumidzi yapafupi, kuti ndikalalikire+ kumenekonso, pakuti ndicho cholinga chimene ndinabwerera.”+