45 Koma atachoka, munthu uja anayamba kulengeza zimenezo paliponse ndi kufalitsa nkhaniyo m’madera ena, moti Yesu sanathenso kulowa mumzinda uliwonse moonekera, koma anapitiriza kukhala kunja kopanda anthu. Komabe anthu anali kubwerabe kuchokera kumbali zonse.+