-
Maliko 6:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Sabata itafika, iye anayamba kuphunzitsa m’sunagoge. Anthu ambiri amene anali kumvetsera, anadabwa ndipo anali kunena kuti: “Kodi munthu ameneyu anazitenga kuti zinthu zimenezi?+ Ndipo n’chifukwa chiyani nzeru zimenezi zinaperekedwa kwa munthu ameneyu, ndi kuti azitha kuchita ntchito zamphamvu zoterezi?
-