Maliko 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ena anali kunena kuti: “Ndi Eliya.”+ Ndipo ena anali kunena kuti: “Ndi mneneri monga analili aneneri ena.”+
15 Koma ena anali kunena kuti: “Ndi Eliya.”+ Ndipo ena anali kunena kuti: “Ndi mneneri monga analili aneneri ena.”+