Maliko 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho Herodiya anam’sungira chidani mumtima+ ndipo anali kufuna kumupha, koma sanathe kutero.+
19 Choncho Herodiya anam’sungira chidani mumtima+ ndipo anali kufuna kumupha, koma sanathe kutero.+