Maliko 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo mwana wamkazi wa Herodiya analowa ndi kuvina, moti anasangalatsa Herode ndi ena amene anali kudya+ naye limodzi. Tsopano mfumu inauza mtsikanayo kuti: “Upemphe kwa ine chilichonse chimene ukufuna, ndipo ndidzakupatsa.” Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:22 Nsanja ya Olonda,3/15/1994, tsa. 30
22 Ndipo mwana wamkazi wa Herodiya analowa ndi kuvina, moti anasangalatsa Herode ndi ena amene anali kudya+ naye limodzi. Tsopano mfumu inauza mtsikanayo kuti: “Upemphe kwa ine chilichonse chimene ukufuna, ndipo ndidzakupatsa.”