Maliko 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho anatuluka n’kukafunsa mayi ake kuti: “Ndikapemphe chiyani?” Mayi akewo anamuuza kuti: “Kapemphe mutu wa Yohane m’batizi.”+
24 Choncho anatuluka n’kukafunsa mayi ake kuti: “Ndikapemphe chiyani?” Mayi akewo anamuuza kuti: “Kapemphe mutu wa Yohane m’batizi.”+