Maliko 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Choncho, nthawi yomweyo mfumu inatumiza msilikali ndi kumulamula kuti abweretse mutuwo. Iye anapita ndi kukamudula mutu m’ndendemo,+
27 Choncho, nthawi yomweyo mfumu inatumiza msilikali ndi kumulamula kuti abweretse mutuwo. Iye anapita ndi kukamudula mutu m’ndendemo,+