Maliko 6:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Kenako mwamsanga, Yesu analimbikitsa ophunzira ake kuti akwere ngalawa ndi kutsogola kupita kutsidya lina loyang’anizana nalo cha ku Betsaida. Koma iye anatsalira akuuza anthuwo kuti azipita kwawo.+
45 Kenako mwamsanga, Yesu analimbikitsa ophunzira ake kuti akwere ngalawa ndi kutsogola kupita kutsidya lina loyang’anizana nalo cha ku Betsaida. Koma iye anatsalira akuuza anthuwo kuti azipita kwawo.+