Maliko 6:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Madzulo mdima utagwa, ngalawa ija inali pakati pa nyanja, koma iye anali yekha kumtunda.+