Maliko 6:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pamenepo Yesu anakwera nawo m’ngalawamo, ndipo mphepoyo inaleka. Ataona izi anadabwa kwambiri mumtima mwawo.+
51 Pamenepo Yesu anakwera nawo m’ngalawamo, ndipo mphepoyo inaleka. Ataona izi anadabwa kwambiri mumtima mwawo.+