Maliko 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno anauza anthuwo kuti akhale pansi. Kenako, anatenga mitanda 7 ya mkate ija, ndi kuyamika.+ Atatero anainyemanyema n’kupatsa ophunzira ake kuti agawe, ndipo iwo anagawira khamu la anthulo.+
6 Ndiyeno anauza anthuwo kuti akhale pansi. Kenako, anatenga mitanda 7 ya mkate ija, ndi kuyamika.+ Atatero anainyemanyema n’kupatsa ophunzira ake kuti agawe, ndipo iwo anagawira khamu la anthulo.+