Maliko 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho anadzuma mowawidwa mtima+ ndi kunena kuti: “N’chifukwa chiyani m’badwo umenewu ukufunitsitsa chizindikiro? Ndithu ndikukuuzani, M’badwo umenewu sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse.”+
12 Choncho anadzuma mowawidwa mtima+ ndi kunena kuti: “N’chifukwa chiyani m’badwo umenewu ukufunitsitsa chizindikiro? Ndithu ndikukuuzani, M’badwo umenewu sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse.”+