Maliko 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo kunachita mtambo ndipo unawaphimba. Kenako mumtambomo munatuluka mawu+ akuti: “Uyu ndiye Mwana wanga+ wokondedwa, muzimumvera.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:7 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,5/2018, tsa. 4
7 Pamenepo kunachita mtambo ndipo unawaphimba. Kenako mumtambomo munatuluka mawu+ akuti: “Uyu ndiye Mwana wanga+ wokondedwa, muzimumvera.”+