Maliko 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Wina m’khamulo anamuyankha kuti: “Mphunzitsi, ine ndabweretsa mwana wanga wamwamuna kwa inu chifukwa ali ndi mzimu womulepheretsa kulankhula.+
17 Wina m’khamulo anamuyankha kuti: “Mphunzitsi, ine ndabweretsa mwana wanga wamwamuna kwa inu chifukwa ali ndi mzimu womulepheretsa kulankhula.+